Salimo 147:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muimbireni Iye amene amaphimba mapiri ndi mitambo,+Amene amakonza mvula kuti igwe padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu wobiriwira m’mapiri.+
8 Muimbireni Iye amene amaphimba mapiri ndi mitambo,+Amene amakonza mvula kuti igwe padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu wobiriwira m’mapiri.+