Salimo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+ Salimo 98:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+
33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+
4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+