Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+ Oweruza 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atangomuona, anayamba kung’amba zovala zake+ ndi kunena kuti: “Kalanga ine mwana wanga! Wandiweramitsa ndi chisoni ndipo ine ndikukupitikitsa. Ndatsegula pakamwa panga pamaso pa Yehova, ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+
35 Atangomuona, anayamba kung’amba zovala zake+ ndi kunena kuti: “Kalanga ine mwana wanga! Wandiweramitsa ndi chisoni ndipo ine ndikukupitikitsa. Ndatsegula pakamwa panga pamaso pa Yehova, ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+