2 Samueli 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,+Ndinaitana Mulungu wanga.+Pamenepo iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake,+Makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+
7 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,+Ndinaitana Mulungu wanga.+Pamenepo iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake,+Makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+