Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+

      Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+

  • 2 Akorinto 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu Khristu, chikondi cha Mulungu, komanso mzimu woyera umene mukupindula nawo limodzi, zikhale nanu nonsenu.+

  • Aefeso 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena