Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anayankha kuti: “Ndachitira nsanje kwambiri+ inu Yehova Mulungu wa makamu, chifukwa ana a Isiraeli asiya pangano lanu.+ Agwetsa maguwa anu ansembe,+ ndipo apha aneneri anu ndi lupanga,+ moti ine ndatsala ndekhandekha.+ Tsopano ayambanso kundifunafuna kuti achotse moyo wanga.”+

  • Salimo 119:139
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 139 Changu changa chandidya,+

      Chifukwa adani anga aiwala mawu anu.+

  • Mateyu 21:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako Yesu analowa m’kachisi ndi kuthamangitsa onse ogulitsa ndi ogula m’kachisimo, ndipo anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndi mabenchi a ogulitsa nkhunda.+

  • Maliko 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano anafika ku Yerusalemu. Kumeneko analowa m’kachisi n’kuyamba kuthamangitsa ogula ndi ogulitsa m’kachisimo. Anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndiponso mabenchi a ogulitsa nkhunda.+

  • Yohane 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena, kuti amati: “Kudzipereka kwambiri panyumba yanu kudzandidya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena