Yesaya 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukamadzadutsa pamadzi,+ ine ndidzakhala nawe.+ Ukamadzawoloka mitsinje, madzi sadzakumiza.+ Ukamadzayenda pamoto sudzapsa ndipo ngakhale lawi la moto silidzakuwaula.+
2 Ukamadzadutsa pamadzi,+ ine ndidzakhala nawe.+ Ukamadzawoloka mitsinje, madzi sadzakumiza.+ Ukamadzayenda pamoto sudzapsa ndipo ngakhale lawi la moto silidzakuwaula.+