Salimo 109:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndasautsika ndipo ndasauka,+Mtima wanga walasika mkati mwanga.+