Salimo 35:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amatsegula kwambiri pakamwa pawo kuti atsutsane nane.+Iwo amati: “Eya! Eya! Tadzionera tokha.”+ Salimo 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onse amene akunena kuti: “Eyaa! Eyaa!”+Ayang’anitsitse modabwa chifukwa cha manyazi awo.+