Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+