Ekisodo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+ 2 Mbiri 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndi mulungu uti pa milungu ya mitundu imeneyi, yomwe makolo anga anaiwononga, yemwe anatha kupulumutsa anthu ake m’manja mwanga, kuti Mulungu wanu athe kukupulumutsani m’manja mwanga?+ Yesaya 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+
14 Ndi mulungu uti pa milungu ya mitundu imeneyi, yomwe makolo anga anaiwononga, yemwe anatha kupulumutsa anthu ake m’manja mwanga, kuti Mulungu wanu athe kukupulumutsani m’manja mwanga?+
23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+