Salimo 147:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amathandiza anthu ofatsa,+Koma anthu oipa amawagwetsera pansi.+ Miyambo 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Onyoza,+ iye amawanyoza,+ koma ofatsa amawakomera mtima.+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+