-
Danieli 3:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Pamenepo Nebukadinezara anapsera mtima Sadirake, Mesake ndi Abedinego ndipo nkhope yake inasintha. Iye analamula kuti ng’anjoyo aisonkhezere kuwirikiza ka 7 kuposa mmene anali kuchitira nthawi zonse.
-
-
Danieli 3:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Pamenepo Nebukadinezara anati: “Atamandike Mulungu wa Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ amene anatumiza mngelo wake+ ndi kupulumutsa atumiki ake amene anamudalira+ ndiponso amene sanamvere mawu a mfumu, koma anali okonzeka kufa chifukwa sanafune kutumikira+ ndi kulambira+ mulungu wina aliyense kupatulapo Mulungu wawo.+
-