Numeri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chigawo cha mafuko atatu cha Efuraimu+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumadzulo. Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi. Salimo 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+ Yesaya 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+
18 “Chigawo cha mafuko atatu cha Efuraimu+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumadzulo. Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi.
23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+
13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+