Salimo 89:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Odala ndi anthu amene amafuula mosangalala.+Iwo amayendabe m’kuwala kwa nkhope yanu, inu Yehova.+