Salimo 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi munthu wolungama angachite chiyaniMaziko achilungamo atagumulidwa?”+ Salimo 75:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziko lapansi ndi onse okhala mmenemo anayamba kusungunuka chifukwa cha mantha,+Ndine amene ndinakonzanso zipilala zake.”+ [Seʹlah.] Miyambo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+
3 Dziko lapansi ndi onse okhala mmenemo anayamba kusungunuka chifukwa cha mantha,+Ndine amene ndinakonzanso zipilala zake.”+ [Seʹlah.]
4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+