Salimo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndikuitana inu Yehova.+Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+Kuti musakhale chete pamaso panga,+Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+ Salimo 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu Yehova, mwaona zimenezi+ ndipo musakhale chete.+Musakhale patali ndi ine, inu Yehova.+ Salimo 109:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 109 Inu Mulungu amene ndimakutamandani,+ musakhale chete.+
28 Ndikuitana inu Yehova.+Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+Kuti musakhale chete pamaso panga,+Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+