Salimo 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+
48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+