1 Mbiri 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Davide anauza atsogoleri a Alevi kuti aike m’malo awo abale awo oimba+ okhala ndi zipangizo zoimbira.+ Zipangizozo zinali zoimbira za zingwe,+ azeze,+ ndi zinganga.+ Anawauza kuti aimbe mokweza kuti nyimbo zachisangalalo zimveke. Salimo 68:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Oimba nyimbo anali patsogolo, oimba zoimbira za zingwe anali pambuyo pawo,+Pakati panali atsikana akuimba maseche.+ Salimo 150:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+
16 Tsopano Davide anauza atsogoleri a Alevi kuti aike m’malo awo abale awo oimba+ okhala ndi zipangizo zoimbira.+ Zipangizozo zinali zoimbira za zingwe,+ azeze,+ ndi zinganga.+ Anawauza kuti aimbe mokweza kuti nyimbo zachisangalalo zimveke.
25 Oimba nyimbo anali patsogolo, oimba zoimbira za zingwe anali pambuyo pawo,+Pakati panali atsikana akuimba maseche.+
4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+