Yobu 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye amayandikira kudzenje,+Ndipo moyo wake umayandikira kwa akupha. Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+