1 Mafumu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Solomo anakhala wolamulira wa maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti, n’kukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumu amenewa anali kubweretsa mphatso kwa Solomo ndi kum’tumikira masiku onse a moyo wake.+ Salimo 80:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pang’onopang’ono nthambi zake zinafika kunyanja,+Ndipo mphukira zake zinafika ku Mtsinje.*+
21 Solomo anakhala wolamulira wa maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti, n’kukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumu amenewa anali kubweretsa mphatso kwa Solomo ndi kum’tumikira masiku onse a moyo wake.+