2 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu. 1 Mafumu 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+ Miyambo 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+
14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu.
31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+
24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+