Aroma 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye tinene kuti chiyani? Kodi Mulungu alibe chilungamo?+ Ayi si zimenezo!