1 Akorinto 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti Malemba amati: “Ndidzathetsa nzeru zonse za anthu anzeru,+ ndipo ndidzakankhira pambali+ kuchenjera kwa anthu ophunzira.”+ 1 Akorinto 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiponso: “Yehova amadziwa kuti maganizo a anthu anzeru ndi opanda pake.”+
19 Pakuti Malemba amati: “Ndidzathetsa nzeru zonse za anthu anzeru,+ ndipo ndidzakankhira pambali+ kuchenjera kwa anthu ophunzira.”+