Genesis 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7. Analipatula kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli, iye wakhala akupuma pa ntchito yake yonse yolenga ndi yopanga zimene anafuna.+ Aheberi 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti, ‘Sadzalowa+ mu mpumulo wanga.’”+
3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7. Analipatula kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli, iye wakhala akupuma pa ntchito yake yonse yolenga ndi yopanga zimene anafuna.+