Salimo 67:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Pakuti inu mudzaweruza anthu molungama.+Ndipo mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. [Seʹlah.] Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+
4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Pakuti inu mudzaweruza anthu molungama.+Ndipo mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. [Seʹlah.]