Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa ndi kum’pereka nsembe yopsereza, nsembe yathunthu,+ kwa Yehova. Atatero anayamba kupempherera Aisiraeli+ kwa Yehova kuti awathandize, ndipo Yehova anamuyankha.+

  • 1 Samueli 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choncho Samueli anafuulira Yehova,+ moti Yehova anadzetsa mabingu ndi mvula tsiku limenelo.+ Pamenepo anthu onse anachita mantha kwambiri ndi Yehova ndiponso ndi Samueli.

  • Yeremiya 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova anandiuza kuti: “Ngakhale Mose+ ndi Samueli+ akanaima pamaso panga, anthu awa sindikanawakomera mtima.+ Ndikanawapitikitsa pamaso panga kuti achoke.+

  • Aheberi 11:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena