1 Samueli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anali kuchita zinthu mwanzeru+ nthawi zonse m’njira zake zonse, ndipo Yehova anali naye.+ 2 Mbiri 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake.
20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake.