Salimo 61:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mtima wanga ukalefuka, ndidzafuulira inu, kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+Nditsogolereni ndi kundikweza pamwamba pa thanthwe lalitali kuposa msinkhu wanga.+ Salimo 142:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinapitirizabe kumukhuthulira nkhawa zanga.+Ndinapitirizabe kumuuza masautso anga.+
2 Mtima wanga ukalefuka, ndidzafuulira inu, kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+Nditsogolereni ndi kundikweza pamwamba pa thanthwe lalitali kuposa msinkhu wanga.+