Salimo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tetezani moyo wanga ndi kundilanditsa.+Musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndathawira kwa inu.+ Salimo 91:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+
20 Tetezani moyo wanga ndi kundilanditsa.+Musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndathawira kwa inu.+
2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+