Aheberi 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mudzapindapinda zinthu zimenezi ngati mkanjo,+ ndipo zidzasinthidwa ngati malaya akunja. Koma inu simudzasintha, ndipo zaka za moyo wanu sizidzatha.”+
12 Mudzapindapinda zinthu zimenezi ngati mkanjo,+ ndipo zidzasinthidwa ngati malaya akunja. Koma inu simudzasintha, ndipo zaka za moyo wanu sizidzatha.”+