1 Mbiri 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Funafunani Yehova ndiponso mphamvu zake,+Funafunani nkhope yake+ nthawi zonse. Salimo 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtima wanga wanena lamulo lanu lakuti: “Ndifunefuneni anthu inu.”+Ndidzakufunafunani, inu Yehova.+