Genesis 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo. Genesis 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Amidiyani aja anakagulitsa Yosefe ku Iguputo kwa Potifara. Potifara anali nduna ya panyumba ya Farao,+ ndiponso anali mkulu wa asilikali olondera mfumu.+ Genesis 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma musadzimvere chisoni+ kapena kudzipsera mtima kuti munandigulitsa kuno. Mulungu ndiye ananditumiza patsogolo panu kuti ndidzapulumutse miyoyo yanu.+ Genesis 50:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu munali ndi cholinga chondichitira zoipa. Koma Mulungu anali ndi cholinga chabwino, kuti apulumutse miyoyo ya anthu ambiri ngati mmene akuchitira panomu.+ Machitidwe 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+
28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.
36 Amidiyani aja anakagulitsa Yosefe ku Iguputo kwa Potifara. Potifara anali nduna ya panyumba ya Farao,+ ndiponso anali mkulu wa asilikali olondera mfumu.+
5 Koma musadzimvere chisoni+ kapena kudzipsera mtima kuti munandigulitsa kuno. Mulungu ndiye ananditumiza patsogolo panu kuti ndidzapulumutse miyoyo yanu.+
20 Inu munali ndi cholinga chondichitira zoipa. Koma Mulungu anali ndi cholinga chabwino, kuti apulumutse miyoyo ya anthu ambiri ngati mmene akuchitira panomu.+
9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+