Ekisodo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao pakuti ndalola iye pamodzi ndi atumiki ake kuumitsa mitima yawo,+ kuti ndichite zizindikiro zanga pamaso pake.+ Aroma 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+
10 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao pakuti ndalola iye pamodzi ndi atumiki ake kuumitsa mitima yawo,+ kuti ndichite zizindikiro zanga pamaso pake.+
18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+