Ekisodo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tiyeni tiwachenjerere,+ kuti asapitirize kuchulukana kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu ndi kumenyana nafe n’kuchoka m’dziko lino.” Machitidwe 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumu imeneyi inagwiritsa ntchito ulamuliro wake molakwika pofuna kuzunza anthu a fuko lathu,+ ndipo mwankhanza inachititsa makolo athuwo kutaya makanda awo, kuti asakhale ndi moyo.+
10 Tiyeni tiwachenjerere,+ kuti asapitirize kuchulukana kuopera kuti pa nthawi ya nkhondo angadzagwirizane ndi adani athu ndi kumenyana nafe n’kuchoka m’dziko lino.”
19 Mfumu imeneyi inagwiritsa ntchito ulamuliro wake molakwika pofuna kuzunza anthu a fuko lathu,+ ndipo mwankhanza inachititsa makolo athuwo kutaya makanda awo, kuti asakhale ndi moyo.+