Ekisodo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma galu sadzauwa aliyense wa ana a Isiraeli, sadzauwa munthu kapena chiweto,+ kuti mudziwe kuti Yehova akhoza kuchitira ana a Isiraeli zinthu zosiyana ndi zimene angachitire Aiguputo.’+ Ekisodo 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho Aiguputo anaumiriza anthuwo kuti achoke m’dzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+
7 Koma galu sadzauwa aliyense wa ana a Isiraeli, sadzauwa munthu kapena chiweto,+ kuti mudziwe kuti Yehova akhoza kuchitira ana a Isiraeli zinthu zosiyana ndi zimene angachitire Aiguputo.’+
33 Choncho Aiguputo anaumiriza anthuwo kuti achoke m’dzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+