1 Mafumu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’zombomo, Hiramu ankatumizamo antchito ake+ omwe anali amalinyero odziwa za panyanja, pamodzi ndi antchito a Solomo. Ezekieli 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘“Anthu okupalasa akupititsa pamadzi ozama.+ Mphepo ya kum’mawa yakuwononga pakatikati pa nyanja.+
27 M’zombomo, Hiramu ankatumizamo antchito ake+ omwe anali amalinyero odziwa za panyanja, pamodzi ndi antchito a Solomo.
26 “‘“Anthu okupalasa akupititsa pamadzi ozama.+ Mphepo ya kum’mawa yakuwononga pakatikati pa nyanja.+