Yobu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iwo amafufuzafufuza mu mdima+ mopanda kuwala,Kuti awachititse kuyendayenda ngati munthu woledzera.+ Yesaya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+
25 Iwo amafufuzafufuza mu mdima+ mopanda kuwala,Kuti awachititse kuyendayenda ngati munthu woledzera.+
14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+