Salimo 60:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pokhala woyera, Mulungu walankhula kuti:+“Ndidzakondwa ndi kupereka Sekemu ngati gawo la cholowa.+Ndipo ndidzayezera anthu anga chigwa cha Sukoti.+
6 Pokhala woyera, Mulungu walankhula kuti:+“Ndidzakondwa ndi kupereka Sekemu ngati gawo la cholowa.+Ndipo ndidzayezera anthu anga chigwa cha Sukoti.+