Deuteronomo 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+ Salimo 60:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinu Mulungu amene mungatichititse kupambana! Koma onani tsopano mwatitaya,+Ndipo inu Mulungu wathu, simukupita kunkhondo pamodzi ndi magulu athu ankhondo.+
14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+
10 Ndinu Mulungu amene mungatichititse kupambana! Koma onani tsopano mwatitaya,+Ndipo inu Mulungu wathu, simukupita kunkhondo pamodzi ndi magulu athu ankhondo.+