2 Samueli 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ponyoza, Simeyi anali kunena kuti: “Choka, choka, munthu wa mlandu wamagazi+ ndi wopanda pake iwe!+ Hoseya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu amalankhula mabodza okhaokha kwa ine.+ Kulikonse kumene ndingayang’ane ndikuona chinyengo cha Isiraeli, koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu+ ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”
7 Ponyoza, Simeyi anali kunena kuti: “Choka, choka, munthu wa mlandu wamagazi+ ndi wopanda pake iwe!+
12 “Efuraimu amalankhula mabodza okhaokha kwa ine.+ Kulikonse kumene ndingayang’ane ndikuona chinyengo cha Isiraeli, koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu+ ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”