Machitidwe 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’buku la Masalimo analembamo kuti, ‘Malo ake okhala asanduke bwinja, ndipo pasapezeke aliyense wokhalamo,’+ komanso kuti, ‘Udindo wake monga woyang’anira utengedwe ndi munthu wina.’+
20 M’buku la Masalimo analembamo kuti, ‘Malo ake okhala asanduke bwinja, ndipo pasapezeke aliyense wokhalamo,’+ komanso kuti, ‘Udindo wake monga woyang’anira utengedwe ndi munthu wina.’+