Salimo 73:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho kudzikuza kuli ngati mkanda m’khosi mwawo,+Ndipo avala chiwawa ngati malaya.+