Salimo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Adani anga onse adzachita manyazi kwambiri+ ndipo adzasokonezeka.Adzabwerera, ndipo nthawi yomweyo adzachita manyazi.+ Salimo 35:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+ Salimo 132:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adani ake ndidzawaveka manyazi,+Koma ufumu*+ wake udzapita patsogolo.”+
10 Adani anga onse adzachita manyazi kwambiri+ ndipo adzasokonezeka.Adzabwerera, ndipo nthawi yomweyo adzachita manyazi.+
26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+