21 (Pakuti pali amuna ena amene akhala ansembe popanda lumbiro, koma pali mmodzi amene wakhala wansembe mwa lumbiro. Lumbiro limeneli ndi la Iye amene ananena za wansembeyo kuti: “Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo) kuti, ‘Iwe ndiwe wansembe mpaka muyaya.’”)+