Salimo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+Yembekezera Yehova.+ Salimo 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu,+Inu nonse amene mukuyembekezera Yehova.+