Ekisodo 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zaka 430 zimenezi zitatha, pa tsiku lomwe zinatha, makamu onse a Yehova anatuluka m’dziko la Iguputo.+ Ekisodo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lino limene munatuluka mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova anakutulutsani mmenemo ndi mphamvu ya dzanja lake.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+
41 Zaka 430 zimenezi zitatha, pa tsiku lomwe zinatha, makamu onse a Yehova anatuluka m’dziko la Iguputo.+
3 Chotero Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lino limene munatuluka mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova anakutulutsani mmenemo ndi mphamvu ya dzanja lake.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+