Yesaya 64:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munatsikira pansi pano pamene munachita zinthu zochititsa mantha+ zimene sitinali kuyembekezera. Mapiri anagwedezeka chifukwa cha inu.+
3 Inu munatsikira pansi pano pamene munachita zinthu zochititsa mantha+ zimene sitinali kuyembekezera. Mapiri anagwedezeka chifukwa cha inu.+