Mika 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu imvani zimene Yehova akunena.+ Nyamukani mukanene mlandu wanu kwa mapiri ndipo zitunda zikamve mawu anu.+ Nahumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+ Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+
6 Anthu inu imvani zimene Yehova akunena.+ Nyamukani mukanene mlandu wanu kwa mapiri ndipo zitunda zikamve mawu anu.+
5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+ Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+