1 Mbiri 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Njenjemerani ndi mantha* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi!Ndiponso dziko lapansi ndi lokhazikika,Silidzagwedezeka ku nthawi zonse.+ Yobu 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amachititsa dziko lapansi kunjenjemera pamalo ake,Mwakuti zipilala+ zake zimagwedezeka. Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+ Salimo 97:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mphezi zake zinawalitsa dziko lapansi.+Dziko linaona ndipo linachita mantha kwambiri.+
30 Njenjemerani ndi mantha* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi!Ndiponso dziko lapansi ndi lokhazikika,Silidzagwedezeka ku nthawi zonse.+
18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+